Mtedza Mtedza kucheza ndi Richard Chipuwa – 1 July 2026

Times 360 Malawi

Peter Fote kucheza ndi Richard Chipuwa, goloboyi wopuma wa Flames ndi Wanderers, akulongosola ulendo wake wa mpira wa zaka 15